Ekisodo 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ana a Gerisoni anali Libini ndi Simeyi,+ malinga ndi mzere wobadwira wa makolo awo.+ Numeri 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ana a Gerisoni, malinga ndi mayina a mabanja awo, anali Libini ndi Simeyi.+