Numeri 33:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Kenako ananyamukanso ku Alimoni-dibilataimu,+ n’kukamanga msasa kumapiri a Abarimu,+ pafupi ndi Nebo.+ Deuteronomo 32:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 “Kwera m’phiri ili la Abarimu,+ phiri la Nebo,+ limene lili m’dziko la Mowabu, moyang’anana ndi Yeriko, ndipo uone dziko la Kanani limene ndikupereka kwa ana a Isiraeli kuti likhale lawo.+
47 Kenako ananyamukanso ku Alimoni-dibilataimu,+ n’kukamanga msasa kumapiri a Abarimu,+ pafupi ndi Nebo.+
49 “Kwera m’phiri ili la Abarimu,+ phiri la Nebo,+ limene lili m’dziko la Mowabu, moyang’anana ndi Yeriko, ndipo uone dziko la Kanani limene ndikupereka kwa ana a Isiraeli kuti likhale lawo.+