Levitiko 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Nyama iliyonse yachilema musaipereke nsembe,+ chifukwa Mulungu sadzakuyanjani. Levitiko 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Isakhale yakhungu, yothyoka chiwalo, yotemeka, yokhala ndi njerewere, nkhanambo kapena zipere.+ Iliyonse yokhala ndi zimenezi musaipereke kwa Yehova ndipo musaike nsembe yotentha ndi moto+ ya nyama zoterezi paguwa lansembe la Yehova. Deuteronomo 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Akakhala ndi vuto, monga kulumala kapena khungu, kapena chilema chilichonse chachikulu, usamam’pereke nsembe kwa Yehova Mulungu wako.+
22 Isakhale yakhungu, yothyoka chiwalo, yotemeka, yokhala ndi njerewere, nkhanambo kapena zipere.+ Iliyonse yokhala ndi zimenezi musaipereke kwa Yehova ndipo musaike nsembe yotentha ndi moto+ ya nyama zoterezi paguwa lansembe la Yehova.
21 Akakhala ndi vuto, monga kulumala kapena khungu, kapena chilema chilichonse chachikulu, usamam’pereke nsembe kwa Yehova Mulungu wako.+