-
Levitiko 23:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Popereka mitanda ya mkateyi muziperekanso ana a nkhosa amphongo opanda chilema okwana 7,+ aliyense wa chaka chimodzi, komanso ng’ombe imodzi yaing’ono yamphongo, ndi nkhosa ziwiri zamphongo. Zimenezi ziziperekedwa monga nsembe yopsereza, nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova. Ziziperekedwa pamodzi ndi nsembe yambewu, ndi nsembe zachakumwa kuti zikhale fungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova.
-