Numeri 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Aliyense amene wakhudza mtembo wa munthu amene waphedwa ndi lupanga,+ kapena mtembo uliwonse, kapenanso fupa la munthu,+ ngakhalenso manda a munthu, akhale wodetsedwa masiku 7.
16 Aliyense amene wakhudza mtembo wa munthu amene waphedwa ndi lupanga,+ kapena mtembo uliwonse, kapenanso fupa la munthu,+ ngakhalenso manda a munthu, akhale wodetsedwa masiku 7.