Numeri 21:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Choncho tiyeni tiwalase.Ndithu Hesiboni adzafafanizika mpaka ku Diboni,+Amayi adzaphedwa mpaka ku Nofa, amuna mpaka ku Medeba.”+ Yoswa 13:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Cholowa chawo chinayambira kumzinda wa Aroweli+ umene uli m’mphepete mwa chigwa cha Arinoni,+ ndiponso mzinda umene uli pakati pa chigwacho, kuphatikizapo malo onse okwererapo a Medeba+ mpaka kukafika ku Diboni.+
30 Choncho tiyeni tiwalase.Ndithu Hesiboni adzafafanizika mpaka ku Diboni,+Amayi adzaphedwa mpaka ku Nofa, amuna mpaka ku Medeba.”+
9 Cholowa chawo chinayambira kumzinda wa Aroweli+ umene uli m’mphepete mwa chigwa cha Arinoni,+ ndiponso mzinda umene uli pakati pa chigwacho, kuphatikizapo malo onse okwererapo a Medeba+ mpaka kukafika ku Diboni.+