Numeri 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atafika kuchigwa* cha Esikolo,+ anadula nthambi yokhala ndi tsango limodzi la mphesa,+ ndipo anthu awiri analinyamula paphewa ndi mitengo yonyamulira. Anatengakonso makangaza*+ ndi nkhuyu. Deuteronomo 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Choncho iwo ananyamuka ndi kupita kulowa m’dera lamapiri.+ Anayenda mpaka anafika m’chigwa* cha Esikolo,+ ndipo anazonda dzikolo.
23 Atafika kuchigwa* cha Esikolo,+ anadula nthambi yokhala ndi tsango limodzi la mphesa,+ ndipo anthu awiri analinyamula paphewa ndi mitengo yonyamulira. Anatengakonso makangaza*+ ndi nkhuyu.
24 Choncho iwo ananyamuka ndi kupita kulowa m’dera lamapiri.+ Anayenda mpaka anafika m’chigwa* cha Esikolo,+ ndipo anazonda dzikolo.