Oweruza 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Gidiyoni anayendabe panjira ya anthu okhala m’mahema, mpaka kukafika kum’mawa kwa Noba ndi Yogebeha.+ Kumeneko anathira nkhondo msasa wa adaniwo iwo asanakonzekere.+
11 Gidiyoni anayendabe panjira ya anthu okhala m’mahema, mpaka kukafika kum’mawa kwa Noba ndi Yogebeha.+ Kumeneko anathira nkhondo msasa wa adaniwo iwo asanakonzekere.+