Ekisodo 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Motero ananyamuka ku Sukoti n’kukamanga msasa ku Etamu m’malire a chipululu.+