Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 22:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Kenako, ana a Isiraeli anasamuka kumaloko n’kukamanga msasa m’chipululu cha Mowabu,+ moyang’anana ndi Yeriko patsidya pa mtsinje wa Yorodano.

  • Yoswa 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kenako mfumu ya Yeriko inauzidwa kuti: “Taonani! Amuna ochokera kwa ana a Isiraeli alowa mumzinda wathu usiku uno kudzafufuza dziko lathu.”

  • Aheberi 11:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Mwa chikhulupiriro, makoma a Yeriko anagwa, atawazungulira masiku 7.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena