Numeri 26:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Amene ali ndi anthu ambiri apatsidwe dziko lalikulu monga cholowa chake, ndipo amene ali ndi anthu ochepa apatsidwe dziko laling’ono monga cholowa chake.+ Aliyense apatsidwe cholowacho malinga ndi chiwerengero cha anthu ake.
54 Amene ali ndi anthu ambiri apatsidwe dziko lalikulu monga cholowa chake, ndipo amene ali ndi anthu ochepa apatsidwe dziko laling’ono monga cholowa chake.+ Aliyense apatsidwe cholowacho malinga ndi chiwerengero cha anthu ake.