Genesis 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Onsewa anagwirizana+ ndi kutsetserekera limodzi kuchigwa cha Sidimu,+ ku Nyanja Yamchere.+ Yoswa 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Malire awo a kum’mwera ankayambira kumapeto kwa Nyanja Yamchere,+ kugombe lake la kum’mwera.