Numeri 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Mukhale ndi amuna ena okuthandizani, mwamuna mmodzi pafuko lililonse. Aliyense akhale woti ndi mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+ Numeri 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Amenewa ndiwo osankhidwa a khamu la anthuwo, atsogoleri a mafuko+ a makolo awo. Aliyense wa iwo ndi mtsogoleri wa anthu masauzande mu Isiraeli.”+
4 “Mukhale ndi amuna ena okuthandizani, mwamuna mmodzi pafuko lililonse. Aliyense akhale woti ndi mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+
16 Amenewa ndiwo osankhidwa a khamu la anthuwo, atsogoleri a mafuko+ a makolo awo. Aliyense wa iwo ndi mtsogoleri wa anthu masauzande mu Isiraeli.”+