Genesis 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kuwonjezera pamenepo, ndidzafunsa za magazi anu. Ngati magazi anu akhetsedwa ndi chamoyo chilichonse, chamoyocho chiyenera kuphedwa, ndipo ngati moyo wa munthu wachotsedwa ndi munthu mnzake ndidzaufuna kuchokera kwa iye.+ Ekisodo 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Amene wamenya munthu mpaka munthuyo kufa ayenera kuphedwa ndithu.+ Levitiko 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘Munthu aliyense amene wakantha ndi kupheratu mnzake, nayenso aziphedwa ndithu.+ Deuteronomo 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 akulu a mumzinda wakwawo azitumiza anthu kukam’tenga kumeneko, ndipo azim’pereka m’manja mwa wobwezera magazi kuti afe ndithu.+
5 Kuwonjezera pamenepo, ndidzafunsa za magazi anu. Ngati magazi anu akhetsedwa ndi chamoyo chilichonse, chamoyocho chiyenera kuphedwa, ndipo ngati moyo wa munthu wachotsedwa ndi munthu mnzake ndidzaufuna kuchokera kwa iye.+
12 akulu a mumzinda wakwawo azitumiza anthu kukam’tenga kumeneko, ndipo azim’pereka m’manja mwa wobwezera magazi kuti afe ndithu.+