6 Ngati msinkhu wa munthuyo ndi wapakati pa mwezi umodzi ndi zaka zisanu, akakhala wamwamuna mtengo wake woikidwiratu ndi masekeli asiliva asanu,+ ndipo akakhala wamkazi ndi masekeli asiliva atatu.
16 Mwanayo uzimuwombola ndi dipo akakwanitsa mwezi umodzi kapena kuposerapo. Uzimuwombola ndi mtengo woikidwiratu, masekeli asiliva asanu, malinga ndi sekeli la kumalo oyera,+ lofanana ndi magera+ 20.