Numeri 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ana a Kohati,+ malinga ndi mayina a mabanja awo, anali Amuramu, Izara,+ Heburoni ndi Uziyeli. Numeri 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mwa ana a Kohati, panali banja la Aamuramu, banja la Aizara, banja la Aheburoni ndi banja la Auziyeli. Awa ndiwo anali mabanja a Akohati.+
27 Mwa ana a Kohati, panali banja la Aamuramu, banja la Aizara, banja la Aheburoni ndi banja la Auziyeli. Awa ndiwo anali mabanja a Akohati.+