Ekisodo 25:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mulandirenso kwa iwo zikopa za nkhosa zonyika mu utoto wofiira, zikopa za akatumbu,* matabwa a mthethe,+
5 Mulandirenso kwa iwo zikopa za nkhosa zonyika mu utoto wofiira, zikopa za akatumbu,* matabwa a mthethe,+