Ekisodo 27:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Koma iwe, ulamule ana a Isiraeli kuti akupezere mafuta ounikira oyenga bwino kwambiri a maolivi, kuti nyale ziziyaka nthawi zonse.+ Levitiko 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Lamula ana a Isiraeli kuti akupezere mafuta ounikira+ oyenga bwino kwambiri a maolivi, kuti nyale iziyaka nthawi zonse.+
20 “Koma iwe, ulamule ana a Isiraeli kuti akupezere mafuta ounikira oyenga bwino kwambiri a maolivi, kuti nyale ziziyaka nthawi zonse.+
2 “Lamula ana a Isiraeli kuti akupezere mafuta ounikira+ oyenga bwino kwambiri a maolivi, kuti nyale iziyaka nthawi zonse.+