Genesis 30:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Leya anati: “Ndachita mwayi!” Chotero anatcha mwanayo dzina lakuti Gadi.*+ Genesis 49:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Kunena za Gadi, gulu la achifwamba lidzamuukira, koma iye adzawathira nkhondo, ndipo achifwambawo pothawa iye adzawakantha koopsa.+
19 “Kunena za Gadi, gulu la achifwamba lidzamuukira, koma iye adzawathira nkhondo, ndipo achifwambawo pothawa iye adzawakantha koopsa.+