Numeri 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Uwerenge ana a Levi potsata nyumba ya makolo awo, malinga ndi mabanja awo. Uwerenge mwamuna aliyense kuyambira wamwezi umodzi kupita m’tsogolo.”+ Numeri 4:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Ana a Merari+ uwawerenge malinga ndi mabanja awo, potsata nyumba za makolo awo.
15 “Uwerenge ana a Levi potsata nyumba ya makolo awo, malinga ndi mabanja awo. Uwerenge mwamuna aliyense kuyambira wamwezi umodzi kupita m’tsogolo.”+