-
Numeri 3:39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Alevi onse amene Mose ndi Aroni anawawerenga, pomvera lamulo la Yehova, malinga ndi mabanja awo, amuna onse kuyambira amwezi umodzi kupita m’tsogolo, analipo 22,000.
-