Numeri 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 mwakuti mwamuna wina wagona* naye,+ koma zimenezi n’kukhala zobisika kwa mwamuna wake.+ Ngakhale kuti mkaziyo wadziipitsa ndithu, zingachitike kuti palibe munthu amene angapereke umboni wotsimikizira kuti mkaziyo walakwadi ndipo iye sanagwidwe. Numeri 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma ngati unazembera mwamuna wako pamene uli m’manja mwake,+ mwa kudziipitsa, mwakuti mwamuna wina wagona nawe,*+ . . . ”
13 mwakuti mwamuna wina wagona* naye,+ koma zimenezi n’kukhala zobisika kwa mwamuna wake.+ Ngakhale kuti mkaziyo wadziipitsa ndithu, zingachitike kuti palibe munthu amene angapereke umboni wotsimikizira kuti mkaziyo walakwadi ndipo iye sanagwidwe.
20 Koma ngati unazembera mwamuna wako pamene uli m’manja mwake,+ mwa kudziipitsa, mwakuti mwamuna wina wagona nawe,*+ . . . ”