Levitiko 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova anapitiriza kulankhula ndi Mose kuti: “Uza ansembe, ana a Aroni, kuti, ‘Aliyense wa inu asadziipitse chifukwa cha munthu amene wamwalira pakati pa anthu a mtundu wake.*+
21 Yehova anapitiriza kulankhula ndi Mose kuti: “Uza ansembe, ana a Aroni, kuti, ‘Aliyense wa inu asadziipitse chifukwa cha munthu amene wamwalira pakati pa anthu a mtundu wake.*+