Levitiko 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Komanso azibweretsa ana awiri a njiwa+ kapena ana awiri a nkhunda, malinga ndi zimene iye angakwanitse. Mbalame imodzi ikhale nsembe yamachimo ndipo inayo ikhale nsembe yopsereza.
22 Komanso azibweretsa ana awiri a njiwa+ kapena ana awiri a nkhunda, malinga ndi zimene iye angakwanitse. Mbalame imodzi ikhale nsembe yamachimo ndipo inayo ikhale nsembe yopsereza.