Numeri 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Asilikali ake olembedwa mayina alipo 74,600.+ Numeri 26:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Amenewa ndiwo anali mabanja a Yuda.+ Amuna onse owerengedwa m’mabanja awo analipo 76,500.+