Numeri 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano atsogoleriwo anafika ndi zopereka zawo pamwambo wotsegulira guwa lansembe,+ pa tsiku lodzoza guwalo. Anabweretsa zopereka zawozo kuguwa lansembe. Numeri 7:84 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 84 Potsegulira guwa lansembe,+ pa tsiku limene guwalo linadzozedwa, atsogoleri+ a Isiraeli anapereka izi: Mbale zikuluzikulu zasiliva 12, mbale zolowa zasiliva+ 12, zikho zagolide 12.
10 Tsopano atsogoleriwo anafika ndi zopereka zawo pamwambo wotsegulira guwa lansembe,+ pa tsiku lodzoza guwalo. Anabweretsa zopereka zawozo kuguwa lansembe.
84 Potsegulira guwa lansembe,+ pa tsiku limene guwalo linadzozedwa, atsogoleri+ a Isiraeli anapereka izi: Mbale zikuluzikulu zasiliva 12, mbale zolowa zasiliva+ 12, zikho zagolide 12.