Levitiko 23:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Lankhula ndi ana a Isiraeli, ndipo uwauze kuti, ‘M’mwezi wa 7,+ pa tsiku loyamba m’mweziwo, muzipuma pa ntchito zanu zonse. Limeneli ndi tsiku la chikumbutso, tsiku loliza lipenga,+ tsiku la msonkhano wopatulika.+ Numeri 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “‘Pa tsiku loyamba la mwezi wa 7, muzichita msonkhano wopatulika.+ Musamagwire ntchito yolemetsa yamtundu uliwonse.+ Lizikhala tsiku lanu loliza lipenga.+
24 “Lankhula ndi ana a Isiraeli, ndipo uwauze kuti, ‘M’mwezi wa 7,+ pa tsiku loyamba m’mweziwo, muzipuma pa ntchito zanu zonse. Limeneli ndi tsiku la chikumbutso, tsiku loliza lipenga,+ tsiku la msonkhano wopatulika.+
29 “‘Pa tsiku loyamba la mwezi wa 7, muzichita msonkhano wopatulika.+ Musamagwire ntchito yolemetsa yamtundu uliwonse.+ Lizikhala tsiku lanu loliza lipenga.+