Salimo 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nyamukani, inu Yehova, yang’anizanani naye maso ndi maso woipayo.+M’gonjetseni. Pulumutsani moyo wanga kwa woipayo ndi lupanga lanu.+ Salimo 132:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nyamukani, inu Yehova, kuti mulowe kumalo anu okhalamo,+Inu pamodzi ndi Likasa+ limene mumasonyezera mphamvu zanu.+
13 Nyamukani, inu Yehova, yang’anizanani naye maso ndi maso woipayo.+M’gonjetseni. Pulumutsani moyo wanga kwa woipayo ndi lupanga lanu.+ Salimo 132:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nyamukani, inu Yehova, kuti mulowe kumalo anu okhalamo,+Inu pamodzi ndi Likasa+ limene mumasonyezera mphamvu zanu.+
8 Nyamukani, inu Yehova, kuti mulowe kumalo anu okhalamo,+Inu pamodzi ndi Likasa+ limene mumasonyezera mphamvu zanu.+