Salimo 78:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho Yehova anamva zimenezo ndipo anakwiya.+Moti moto unayakira Yakobo,+Ndipo mkwiyo unatsikira pa Isiraeli.+ Salimo 106:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Moto unayaka pakati pa msonkhano wawo.+Malawi amoto ananyeketsa anthu oipawo.+
21 Choncho Yehova anamva zimenezo ndipo anakwiya.+Moti moto unayakira Yakobo,+Ndipo mkwiyo unatsikira pa Isiraeli.+