Numeri 3:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ntchito yawo+ inali yosamalira likasa,+ tebulo,+ choikapo nyale,+ maguwa ansembe,+ ndi ziwiya+ za m’malo oyerawo zimene anali kutumikira nazo, ndiponso nsalu yotchinga,+ komanso ntchito zonse zokhudza utumikiwu. Numeri 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Akatero, azitenga ziwiya zonse+ zimene amachitira utumiki wawo nthawi zonse m’malo oyera, n’kuzikuta ndi nsalu yabuluu. Ndiyeno aziziphimba ndi zikopa za akatumbu,+ n’kuikako mtengo wake wonyamulira.
31 Ntchito yawo+ inali yosamalira likasa,+ tebulo,+ choikapo nyale,+ maguwa ansembe,+ ndi ziwiya+ za m’malo oyerawo zimene anali kutumikira nazo, ndiponso nsalu yotchinga,+ komanso ntchito zonse zokhudza utumikiwu.
12 Akatero, azitenga ziwiya zonse+ zimene amachitira utumiki wawo nthawi zonse m’malo oyera, n’kuzikuta ndi nsalu yabuluu. Ndiyeno aziziphimba ndi zikopa za akatumbu,+ n’kuikako mtengo wake wonyamulira.