Numeri 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chihema chopatulika chitapasulidwa,+ ana a Gerisoni+ ndi ana a Merari,+ onyamula chihema chopatulikacho, ananyamuka. Numeri 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako Akohati, onyamula zinthu za m’malo opatulika+ ananyamuka, kuti pokafika akapeze chihema chopatulika chitamangidwa kale.
17 Chihema chopatulika chitapasulidwa,+ ana a Gerisoni+ ndi ana a Merari,+ onyamula chihema chopatulikacho, ananyamuka.
21 Kenako Akohati, onyamula zinthu za m’malo opatulika+ ananyamuka, kuti pokafika akapeze chihema chopatulika chitamangidwa kale.