Numeri 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wa fuko la Efuraimu anali Hoshiya,+ mwana wa Nuni. Numeri 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Amenewa ndiwo mayina a amuna amene Mose anawatuma kuti akazonde dzikolo. Mose anatcha Hoshiya mwana wa Nuni kuti Yehoswa.*+
16 Amenewa ndiwo mayina a amuna amene Mose anawatuma kuti akazonde dzikolo. Mose anatcha Hoshiya mwana wa Nuni kuti Yehoswa.*+