Numeri 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aleviwo uwapereke kwa Aroni ndi kwa ana ake. Amenewa ndi amene aperekedwa. Aperekedwa kwa iye kuchokera mwa ana a Isiraeli.+ Numeri 3:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Unditengere Alevi akhale anga m’malo mwa ana aamuna onse oyamba kubadwa a Isiraeli.+ Unditengerenso ziweto zonse za Alevi m’malo mwa ziweto zonse zoyamba kubadwa za ana a Isiraeli.+ Ine ndine Yehova.”
9 Aleviwo uwapereke kwa Aroni ndi kwa ana ake. Amenewa ndi amene aperekedwa. Aperekedwa kwa iye kuchokera mwa ana a Isiraeli.+
41 Unditengere Alevi akhale anga m’malo mwa ana aamuna onse oyamba kubadwa a Isiraeli.+ Unditengerenso ziweto zonse za Alevi m’malo mwa ziweto zonse zoyamba kubadwa za ana a Isiraeli.+ Ine ndine Yehova.”