Numeri 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Ine ndikutenga Alevi pakati pa ana a Isiraeli m’malo mwa ana onse oyamba kubadwa+ a ana a Isiraeli ndipo iwo akhala anga. Numeri 3:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 “Unditengere Alevi akhale anga m’malo mwa ana onse aamuna oyamba kubadwa a Isiraeli. Unditengerenso ziweto za Alevi zikhale zanga m’malo mwa ziweto za Aisiraeli.+ Ine ndine Yehova.
12 “Ine ndikutenga Alevi pakati pa ana a Isiraeli m’malo mwa ana onse oyamba kubadwa+ a ana a Isiraeli ndipo iwo akhala anga.
45 “Unditengere Alevi akhale anga m’malo mwa ana onse aamuna oyamba kubadwa a Isiraeli. Unditengerenso ziweto za Alevi zikhale zanga m’malo mwa ziweto za Aisiraeli.+ Ine ndine Yehova.