Numeri 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aleviwo uwapereke kwa Aroni ndi kwa ana ake. Amenewa ndi amene aperekedwa. Aperekedwa kwa iye kuchokera mwa ana a Isiraeli.+ Numeri 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Amenewa ndi operekedwa. Aperekedwa kwa ine kuchokera pakati pa ana a Isiraeli.+ Ine ndikuwatenga iwowa m’malo mwa onse otsegula mimba ya mayi awo, oyamba kubadwa onse pakati pa ana a Isiraeli.+
9 Aleviwo uwapereke kwa Aroni ndi kwa ana ake. Amenewa ndi amene aperekedwa. Aperekedwa kwa iye kuchokera mwa ana a Isiraeli.+
16 Amenewa ndi operekedwa. Aperekedwa kwa ine kuchokera pakati pa ana a Isiraeli.+ Ine ndikuwatenga iwowa m’malo mwa onse otsegula mimba ya mayi awo, oyamba kubadwa onse pakati pa ana a Isiraeli.+