Yoswa 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kenako Yoswa anawakantha ndi kuwapha. Atatero anawapachika pamitengo isanu, pomwe anakhalapo mpaka madzulo.+ Machitidwe 10:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ndipo ife ndife mboni za zinthu zonse zimene anachita m’dziko la Ayuda ndi mu Yerusalemu momwe. Koma iwo anamupha mwa kumupachika pamtengo.+
26 Kenako Yoswa anawakantha ndi kuwapha. Atatero anawapachika pamitengo isanu, pomwe anakhalapo mpaka madzulo.+
39 Ndipo ife ndife mboni za zinthu zonse zimene anachita m’dziko la Ayuda ndi mu Yerusalemu momwe. Koma iwo anamupha mwa kumupachika pamtengo.+