Mlaliki 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kuli bwino kuti usalonjeze+ kusiyana ndi kulonjeza koma osakwaniritsa zimene walonjezazo.+