Deuteronomo 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Tsopano amenewa ndiwo malamulo, malangizo ndi zigamulo zimene Yehova Mulungu wanu walamula kuti ndikuphunzitseni,+ kuti muzikazitsatira m’dziko limene mukuwolokerako kukalitenga kukhala lanu. Yoswa 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mtundu wonse utangotha kuwoloka mtsinje wa Yorodano,+ Yehova anauza Yoswa kuti:
6 “Tsopano amenewa ndiwo malamulo, malangizo ndi zigamulo zimene Yehova Mulungu wanu walamula kuti ndikuphunzitseni,+ kuti muzikazitsatira m’dziko limene mukuwolokerako kukalitenga kukhala lanu.