Deuteronomo 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mose pamodzi ndi akulu a Isiraeli anapitiriza kuuza anthuwo kuti: “Muzisunga lamulo lililonse limene ndikukupatsani lero.+
27 Mose pamodzi ndi akulu a Isiraeli anapitiriza kuuza anthuwo kuti: “Muzisunga lamulo lililonse limene ndikukupatsani lero.+