Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 9:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Sikuti mukulowa m’dziko ili kukalitenga kukhala lanu chifukwa cha kulungama kwanu+ kapena chifukwa cha kuwongoka mtima kwanu.+ Yehova Mulungu wanu akukankhira mitundu iyi kutali ndi inu, kwenikweni chifukwa cha kuipa kwawo,+ ndiponso kuti Yehova akwaniritse mawu onse amene analumbirira makolo anu Abulahamu,+ Isaki+ ndi Yakobo.+

  • Yoswa 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Pitani mumsasa wonsewu, mukauze anthu kuti, ‘Konzekani ndi kutenga zonse zofunikira, chifukwa pakapita masiku atatu kuchokera lero, mudzawoloka Yorodano uyu, ndi kulowa m’dzikolo kuti mukalilande, dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti likhale lanu.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena