Yona 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako Mulungu woona anatumiza mbozi+ m’bandakucha wa tsiku lotsatira, kuti ikawononge chomera cha mtundu wa mphonda chija, moti chomeracho chinafota.+
7 Kenako Mulungu woona anatumiza mbozi+ m’bandakucha wa tsiku lotsatira, kuti ikawononge chomera cha mtundu wa mphonda chija, moti chomeracho chinafota.+