Deuteronomo 26:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Inu lero mwachititsa Yehova kunena kuti adzakhala Mulungu wanu mukamayenda m’njira zake ndi kusunga malangizo,+ malamulo+ ndi zigamulo zake+ ndiponso kumvera mawu ake.+ Deuteronomo 30:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 moti mwabwerera kwa Yehova Mulungu wanu+ ndi kumvera mawu ake ndi mtima wanu wonse ndi moyo wanu wonse,+ mogwirizana ndi zonse zimene ndikukulamulani lero, inuyo ndi ana anu,
17 Inu lero mwachititsa Yehova kunena kuti adzakhala Mulungu wanu mukamayenda m’njira zake ndi kusunga malangizo,+ malamulo+ ndi zigamulo zake+ ndiponso kumvera mawu ake.+
2 moti mwabwerera kwa Yehova Mulungu wanu+ ndi kumvera mawu ake ndi mtima wanu wonse ndi moyo wanu wonse,+ mogwirizana ndi zonse zimene ndikukulamulani lero, inuyo ndi ana anu,