Deuteronomo 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Koma mukadzaiwala Yehova Mulungu wanu, n’kutsatira milungu ina, kuitumikira ndiponso kuigwadira, ndikukuchitirani umboni lero kuti anthu inu mudzatha.+ Yoswa 23:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mawu onse abwino amene Yehova Mulungu wanu analankhula akwaniritsidwa pa inu,+ momwemonso Yehova adzakwaniritsa pa inu mawu onse oipa, kufikira atakufafanizani kukuchotsani padziko labwinoli, limene Yehova Mulungu wanu wakupatsani.+
19 “Koma mukadzaiwala Yehova Mulungu wanu, n’kutsatira milungu ina, kuitumikira ndiponso kuigwadira, ndikukuchitirani umboni lero kuti anthu inu mudzatha.+
15 Mawu onse abwino amene Yehova Mulungu wanu analankhula akwaniritsidwa pa inu,+ momwemonso Yehova adzakwaniritsa pa inu mawu onse oipa, kufikira atakufafanizani kukuchotsani padziko labwinoli, limene Yehova Mulungu wanu wakupatsani.+