Deuteronomo 27:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘Wotembereredwa ndi munthu amene sadzatsatira mawu a m’chilamulo ichi ndipo sadzawagwiritsa ntchito.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’) Deuteronomo 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu ndi kuonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero, matemberero otsatirawa adzakugwerani ndi kukupezani:+
26 “‘Wotembereredwa ndi munthu amene sadzatsatira mawu a m’chilamulo ichi ndipo sadzawagwiritsa ntchito.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)
15 “Mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu ndi kuonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero, matemberero otsatirawa adzakugwerani ndi kukupezani:+