40 Muzisunga malangizo+ ndi zigamulo zake zimene ndikukulamulani lero. Muzitero kuti nthawi zonse zinthu zikuyendereni bwino,+ inuyo ndi ana anu obwera pambuyo panu, ndiponso kuti mutalikitse masiku anu panthaka imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani.”+