Ekisodo 34:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Dzilembere mawuwa+ chifukwa ine ndikuchita pangano ndi iwe ndi Isiraeli mogwirizana ndi mawu amenewa.”+ Danieli 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Masoka onse amene analembedwa m’chilamulo cha Mose+ atigwera,+ ndipo ife sitinakhazike pansi mtima wanu, inu Yehova Mulungu wathu, mwa kusiya zolakwa zathu+ ndi kusonyeza kuti tikumvetsa kuti ndinu wokhulupirika.+
27 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Dzilembere mawuwa+ chifukwa ine ndikuchita pangano ndi iwe ndi Isiraeli mogwirizana ndi mawu amenewa.”+
13 Masoka onse amene analembedwa m’chilamulo cha Mose+ atigwera,+ ndipo ife sitinakhazike pansi mtima wanu, inu Yehova Mulungu wathu, mwa kusiya zolakwa zathu+ ndi kusonyeza kuti tikumvetsa kuti ndinu wokhulupirika.+