Levitiko 26:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 pamenepo, ineyo ndidzatsutsana nanu,+ ndipo ndidzakukanthani maulendo 7 chifukwa cha machimo anu.+ Deuteronomo 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu ndi kuonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero, matemberero otsatirawa adzakugwerani ndi kukupezani:+
24 pamenepo, ineyo ndidzatsutsana nanu,+ ndipo ndidzakukanthani maulendo 7 chifukwa cha machimo anu.+
15 “Mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu ndi kuonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero, matemberero otsatirawa adzakugwerani ndi kukupezani:+