Numeri 20:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kumeneko, Mose anavula Aroni zovala zake zaunsembe n’kuveka mwana wake Eleazara. Pambuyo pake, Aroni anamwalira pamwamba pa phiripo.+ Potsirizira pake, Mose ndi Eleazara anatsika m’phirimo. Numeri 33:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Wansembe Aroni anakwera m’phiri la Hora monga mmene Yehova anamulamulira, ndipo anamwalira ali m’phirimo. Anamwalira m’chaka cha 40 kuchokera pamene ana a Isiraeli anatuluka m’dziko la Iguputo, m’mwezi wachisanu, pa tsiku loyamba la mweziwo.+
28 Kumeneko, Mose anavula Aroni zovala zake zaunsembe n’kuveka mwana wake Eleazara. Pambuyo pake, Aroni anamwalira pamwamba pa phiripo.+ Potsirizira pake, Mose ndi Eleazara anatsika m’phirimo.
38 Wansembe Aroni anakwera m’phiri la Hora monga mmene Yehova anamulamulira, ndipo anamwalira ali m’phirimo. Anamwalira m’chaka cha 40 kuchokera pamene ana a Isiraeli anatuluka m’dziko la Iguputo, m’mwezi wachisanu, pa tsiku loyamba la mweziwo.+