Levitiko 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Matumbo+ ake ndi ziboda zake azizitsuka ndi madzi. Akatero ansembe azitentha* nyama yonse paguwa lansembe kuti ikhale nsembe yopsereza. Imeneyi ndi nsembe yotentha ndi moto, yafungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova.+ Salimo 51:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mukatero mudzakondwera ndi nsembe zachilungamo,+Mudzakondwera ndi nsembe zopsereza ndi nsembe zathunthu.+Pamenepo ng’ombe zamphongo zidzaperekedwa paguwa lanu la nsembe.+
9 Matumbo+ ake ndi ziboda zake azizitsuka ndi madzi. Akatero ansembe azitentha* nyama yonse paguwa lansembe kuti ikhale nsembe yopsereza. Imeneyi ndi nsembe yotentha ndi moto, yafungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova.+
19 Mukatero mudzakondwera ndi nsembe zachilungamo,+Mudzakondwera ndi nsembe zopsereza ndi nsembe zathunthu.+Pamenepo ng’ombe zamphongo zidzaperekedwa paguwa lanu la nsembe.+