Salimo 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipulumutseni m’kamwa mwa mkango,+Ndipo mundiyankhe ndi kundipulumutsa ku nyanga za ng’ombe zamphongo zam’tchire.+ Salimo 92:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma inu mudzakweza nyanga* yanga ngati nyanga ya ng’ombe yam’tchire yamphongo.*+Ndidzadzola mafuta abwino.+
21 Ndipulumutseni m’kamwa mwa mkango,+Ndipo mundiyankhe ndi kundipulumutsa ku nyanga za ng’ombe zamphongo zam’tchire.+
10 Koma inu mudzakweza nyanga* yanga ngati nyanga ya ng’ombe yam’tchire yamphongo.*+Ndidzadzola mafuta abwino.+